Deuteronomy 4:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi alipo anthu ena amene adakhalabe ndi moyo, atamva mau a Mulungu ali m'moto, monga m'mene mudamvera inu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi pali mtundu wa anthu udamva mau a mulungu wina akunena pakati pa moto, monga mudamva inu, ndi kukhala ndi moyo?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi uliponso mtundu wina wa anthu umene unamva mawu a Mulungu akuyankhula kuchokera mʼmoto nʼkukhala ndi moyo monga mwachitira inumu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi pali mtundu wa anthu udamva a Malungu akunena pakati pa moto, monga mudamva inu, ndi kukhala ndi moyo?