Deuteronomy 4:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene munkayenda, Iye adapirikitsira kutali mitundu ikuluikulu kupambana inu, kuti akuloŵetseni ndi kukupatsani dziko laolo, kumene muli lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kupirikitsa amitundu akulu ndi amphamvu oposa inu pamaso panu, kukulowetsani ndi kukupatsani dziko lao likhale cholowa chanu, monga lero lino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti akupirikitsireni mayiko akuluakulu ndi amphamvu kuposa inu, ndi kukubweretsani inu ku dziko lawo kuti likhale lanu, monga liliri lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kupitikitsa amitundu akuru ndi amphamvu oposa inu pamaso panu, kukulowetsani ndi kukupatsani dziko lao likhale colowa canu, monga lero lino.