Deuteronomy 4:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko limene adalandalo lidayambira ku mudzi wa Aroere pamphepete pa mtsinje wa Arinoni, mpaka kukafika ku phiri la Sirioni (ndiye kuti phiri la Heremoni),
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuyambira ku Aroere, ndiwo m'mphepete mwa mtsinje wa Arinoni, kufikira phiri la Sirioni (ndilo Heremoni),
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko ili linayambira ku Aroeri cha kumphepete kwa khwawa la Arinoni ku phiri la Siyoni (limeneli ndi phiri la Herimoni),
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuyambira ku Aroeri, ndiwo m'mphepete mwa mtsinje wa Arinoni, kufikira phiri la Sioni (ndilo Herimoni),