Deuteronomy 4:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndi dziko lonse la Araba la kuvuma kwa mtsinje wa Yordani, mpaka kukafika ku Nyanja ya Araba, patsinde pa phiri la Pisiga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi chidikha chonse tsidya lija la Yordani kum'mawa, kufikira ku Nyanja ya Araba, pa tsinde lake la Pisiga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndi kuphatikizapo dziko lonse la Araba cha kummawa kwa Yorodani mpaka kukafika ku Nyanja ya Araba, kumunsi kwa Phiri la Pisiga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi cidikha conse tsidya lija la Yordana kum'mawa, kufikira nyanja ya kucidikha, pa tsinde lace la Pisiga.