Deuteronomy 5:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uzisunga tsiku la Sabata ndi kuliyeretsa, monga momwe Ine Chauta, Mulungu wako, ndidakulamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Samalira tsiku la Sabata likhale lopatulika, monga Yehova Mulungu wako anakulamulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uzisunga tsiku la Sabata kuti likhale lopatulika monga momwe Yehova Mulungu wako anakulamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Samalira tsiku la Sabata likhale lopatulika, monga Yehova Mulungu wako anakulamulira.