Deuteronomy 5:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uzigwira ntchito zako zonse ndi kuzitsiriza pa masiku asanu ndi limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Masiku asanu ndi limodzi uzigwiritsa ntchito, ndi kuchita ntchito zako zonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Uzigwira ntchito zako zonse masiku asanu ndi limodzi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Masiku asanu ndi limodzi uzigwiritsa nchito, ndi kucita nchito zako zonse;