Deuteronomy 5:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene mudalankhula ndi ine, Chauta adamva mau anu ndipo adandiwuza kuti, “Ndamva zimene akulankhula anthuzi, ndi zabwino zokhazokha zonsezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anamva mau a kunena kwanu, pamene munanena ndi ine; ndipo Yehova anati kwa ine, Ndidamva mau a kunena kwao kwa anthu awa, amene ananena ndi iwe; chokoma chokhachokha adanenachi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anakumvani pamene munkayankhula kwa ine ndipo Yehova anati kwa ine, “Ndamva zimene anthuwa anena kwa iwe. Chilichonse chimene anena ndi chabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anamva mau a kunena kwanu, pamene munanena ndi ine; ndipo Yehova anati kwa ine, Ndidamva mau a kunena kwao kwa anthu awa, amene ananena ndi iwe; cokoma cokha cokha adanenaci.