Deuteronomy 5:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sikuti chipangano chimenechi adangochita ndi makolo athu okha ai, komanso ndi ife tonse amene tili ndi moyo pano lero lino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova sanachite chipangano ichi ndi makolo athu, koma ndi ife, ife amene tili ndi moyo tonsefe pano lero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova sanachite pangano ndi makolo athu koma ndi ife, tonse amene tili moyo lero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova sanacita cipangano ici ndi makolo athu, koma ndi ife, ife amene tiri ndi moyo tonsefe pane lero.