Deuteronomy 7:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa dziko lapansi, palibe anthu amene adzakhale odala ngati inu. Sipadzaoneka mwamuna kapena mkazi wosabala pakati panu, ndiponso pakati pa zoŵeta zanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzakhala odalitsika koposa mitundu yonse ya anthu; sipadzakhala mwamuna kapena wamkazi wosabala pakati pa inu, kapena pakati pa zoweta zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mudzadalitsika kuposa mtundu wina uliwonse wa anthu ndipo palibe mwamuna kapena mkazi aliyense pakati panu amene adzakhale wosabereka. Ziweto zanu nazonso, sipadzapezeka zosabereka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzakhala odalitsika koposa mitundu yonse ya anthu; sipadzakhala mwamuna kapena wamkazi wosabala pakati pa inu, kapena pakati pa zoweta zanu.