Deuteronomy 7:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musanene kuti anthu ameneŵa achuluka kupambana inu, ndipo kuti simungathe kuŵapirikitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukadzanena m'mtima mwanu, Amitundu awa andichulukira; ndikhoza bwanji kuwapirikitsa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukhoza kunena kuti, “Anthu awa ndi amphamvu kuposa ifeyo. Nanga tingawapirikitse bwanji?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukadzanena m'mtima mwanu, Amitundu awa andicurukira; ndikhoza bwanji kuwapitikitsa?