Deuteronomy 7:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musaŵaope. Kumbukirani zimene Chauta, Mulungu wanu, adam'chita Farao mfumu ya ku Ejipito, pamodzi ndi anthu ake omwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamawaopa; mukumbukire bwino chimene Yehova Mulungu wanu anachitira Farao, ndi Ejipito wonse;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma musachite nawo mantha, kumbukirani bwino zimene Yehova Mulungu wanu anachita ndi Farao pamodzi ndi Igupto yense.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
musamawaopa; mukumbukile bwino cimene Yehova Mulungu wanu anacitira Farao, ndi Aigupto wonse;