Deuteronomy 7:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mukamayenda, Iye adzapirikitsa mitundu imeneyi pang'onopang'ono. Komatu simudzaŵatha onse nthaŵi imodzi. Mukadatero, nyama zakuthengo zikadachuluka ndi kumakuwopsani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova Mulungu wanu adzataya amitundu awa pang'onopang'ono; simuyenera kuwaononga msanga, kuti zingakuchulukireni zilombo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova Mulungu wanu adzapirikitsa anthu a mitundu yonse pamaso panu, pangʼonopangʼono. Sadzakulolani kuti muwathe nthawi imodzi, kuti nyama zakuthengo zingadzaswane mokuzungulirani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova Mulungu wanu adzataya amitundu awa pang'ono pang'ono; simuyenera kuwaononga msanga, kuti zingakucurukireni zirombo.