Deuteronomy 7:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adzapereka adani anuwo kwa inu, ndipo adzaŵasokoneza kwambiri mpaka atatha onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma Yehova Mulungu wanu adzawapereka pamaso panu, nadzawapirikitsa ndi kupirikitsa kwakukulu, kufikira ataonongeka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova Mulungu wanu adzawapereka kwa inu, adzawasokoneza kufikira atawonongedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma Yehova Mulungu wanu adzawapereka pamaso panu, nadzawapitikitsa ndi kupitikitsa kwakukuru, kufikira ataonongeka.