Deuteronomy 7:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafumu onse adzaŵapereka kwa inu. Mudzaŵapha onse, ndipo adzaiŵalika. Palibe amene adzakuletseni, mpaka mudzaŵaononga onsewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzaperekanso mafumu ao m'dzanja mwanu, ndipo muwafafanize maina ao pansi pa thambo; palibe munthu mmodzi adzaima pamaso panu, kufikira mutawaononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzapereka mafumu awo mʼdzanja lanu, ndipo adzafafaniza mayina awo pa dziko lapansi. Palibe amene adzalimbana nanu, inu mudzawawononga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzaperekanso mafumu ao m'dzanja mwanu, ndipo muwafafanize maina ao pansi pa thambo; palibe munthu mmodzi adzaima pamaso panu, kufikira mutawaononga,