Deuteronomy 7:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amenewo mudzaŵachite izi: mudzaphwanye maguwa ao, mudzaphwanye miyala yoimiritsa yopembedzapo, mudzagwetse mafano ao aja a Aserimu, ndipo mudzatenthe mafano ao osema.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma muzichita nao motero: mukapasule maguwa ao a nsembe, ndi kuphwanya zoimiritsa zao, ndi kulikha zifanizo zao, ndi kutentha mafano ao osema ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mukachite izi: Mukagumule maguwa awo ansembe, mukaswe miyala yawo yachipembedzo, mukadule mitengo yawo ya Asera, ndi kutentha mafano awo pa moto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma muzicita nao motero: mukapasule maguwa ao a nsembe, ndi kuphwanya zoimiritsa zao, ndi kulikha zifanizo zao, ndi kutentha mafano ao osema ndi moto.