Deuteronomy 9:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usandiletse, ndikufuna kuŵaononga ndi kufafaniziratu dzina lao pansi pa thambo. Koma iwe ndidzakusandutsa mtundu waukulu ndi wamphamvu kupambana iwoŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
undileke, ndiwaononge, ndi kufafaniza dzina lao pansi pa thambo; ndipo ndidzakuyesa iwe mtundu wa anthu wamphamvu ndi waukulu woposa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndilekeni ndiwawononge ndi kufafaniza mayina awo pa dziko lapansi. Ndipo ndidzakuyesa iwe mtundu wa anthu wamphamvu ndi wochuluka kuposa iwo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
undileke, ndiwaononge, ndi kufafaniza dzina lao pansi pa thambo; ndipo ndidzakuyesa iwe mtundu wa anthu wamphamvu ndi waukuru woposa iwo.