Deuteronomy 9:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo ine ndidaponya pansi miyalayo ndi kuiswa, inu mukuwona.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo ndinagwira magome awiriwo, ndi kuwataya achoke m'manja anga awiri, ndi kuwaswa pamaso panu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero ine ndinaponya pansi miyala imene inali mʼmanja mwanga, ndi kuyiphwanya inu mukuona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinagwira magome awiriwo, ndi kuwataya acoke m'manja anga awiri, ndi kuwaswa pamaso panu.