Deuteronomy 9:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndinkaopa mkwiyo wa Chauta woopsawo, chifukwa kukwiya kwake kunali koti akadakuwonongani. Koma nthaŵi imeneyo Chauta adamvanso pemphero langa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukali, umene Yehova anakwiya nao pa inu kukuonongani. Koma Yehova anandimvera nthawi ijanso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinachita mantha ndi mkwiyo ndi ukali wa Yehova chifukwa anakwiya nanu kokwanira kukuwonongani. Koma Yehova anandimveranso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndinacita mantha cifukwa ca mkwiyo waukali, umene Yehova anakwiya nao pa inu kukuonongani, Koma Yehova anandimvera nthawi ijanso.