Deuteronomy 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adakwiyiranso Aroni, kotero kuti akadamupha ndithu, koma ndidampemphereranso nthaŵi yomweyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anakwiya kwambiri ndi Aroni kumuononga; koma ndinampempherera Aroni nthawi yomweyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yehova anakwiya ndi Aaroni ndipo akanamuwononga, koma ine ndinamupemphereranso Aaroniyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova aliakwiya kwambiri ndi Aroni kumuononga; koma ndinampempherera Aroni nthawi yomweyo.