Deuteronomy 9:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumbukirani atumiki anu aja, Abrahamu, Isaki ndi Yakobe, ndipo musasamale kukanika kwa anthu anuŵa, kuipa kwao ndi kuchimwa kwao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumbukirani atumiki anu, Abrahamu, Isaki, ndi Yakobo; musapenyerera kupulukira kwa anthu awa, kapena choipa chao, kapena tchimo lao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumbukirani atumiki anu Abrahamu, Isake ndi Yakobo. Musatengere kupulupudza, kuyipa ndi kuchimwa kwawo anthuwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumbukilani atumiki anu, Abrahamu, Isake, ndi Yakobo; musapenyerera kupulukira kwa anthu awa, kapena coipa cao, kapena cimo lao;