Deuteronomy 9:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale ku phiri la Horebu kuja, mudakwiyitsa Chauta, kukwiya kwake koti akadakuwonongani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'Horebu momwe munautsa mkwiyo wa Yehova; ndipo Yehova anakwiya nanu kukuonongani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Horebu munaputa mkwiyo wa Yehova, kotero kuti anakwiya kwambiri nafuna kukuwonongani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'Horebe momwe munautsa mkwiyo wa Yehova; ndipo Yehova anakwiya nanu kukuonongani.