Ecclesiastes 10:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chitsiru chimagwira ntchito modzitopetsa, koma njira yopita ku mzinda sichiidziŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ntchito ya zitsiru izitopetsa zonsezo, pakuti sichidziwa kunka kumudzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chitsiru chimatopa msanga ndi ntchito yochepa; ndipo sichikhala ndi mphamvu zobwererera ku mudzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nchito ya zitsiru izitopetsa zonsezo, pakuti sicidziwa kunka kumudzi.