Ecclesiastes 10:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Denga limaloshoka, mwini wake akakhala waulesi, ndipo nyumba imadontha, mwiniwake akakhala nthyamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsindwi litewa ndi mphwai za eni ake; nyumba nidontha ndi ulesi wa manja.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu ndi waulesi, denga lake limaloshoka; ngati manja ake ndi alobodo nyumba yake imadontha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsindwi litewa ndi mphwai za eni ace; nyumba nidontha ndi ulesi wa manja.