Ecclesiastes 10:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Phwando ndi lokondwetsa anthu, ndipo vinyo ndi wosangalatsa moyo. Komatu zonsezo nzolira ndalama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amaphikira zakudya kuti asekere, vinyo nakondweretsa moyo; ndipo ndalama zivomera zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Phwando ndi lokondweretsa anthu, ndipo vinyo ndi wosangalatsa moyo, koma ndalama ndi yankho la chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amaphikira zakudya kuti asekere, vinyo nakondweretsa moyo; ndipo ndalama zibvomera zonse.