Ecclesiastes 10:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wolamula akakukwiyira, usachoke pa ntchito yako, pakuti kufatsa kumakonza ngakhale zolakwa zazikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mkulu akukwiyira, usasiye malo ako; chifukwa chifatso chipembedza utachimwa kwambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati wolamulira akukwiyira, usachoke pa ntchito yako; kufatsa kumakonza zolakwa zazikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mkuru akukwiyira, usasiye malo ako; cifukwa cifatso cipembedza utacimwa kwambiri.