Ecclesiastes 10:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pansi pano pali choipa china chimene ndachiwona, choipa chake ndi cholakwa chimene amachichita wolamula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pali choipa ndachiona pansi pano, ngati kulakwa koyambira ndi mkulu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali choyipa chimene ndinachiona pansi pano, kulakwitsa kumene kumachokera kwa wolamulira:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pali coipa ndaciona pansi pano, ngati kulakwa koyambira ndi mkuru;