Ecclesiastes 11:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndalama zako uzisungize pa malo angapo, malo ambiri ndithu, pakuti sukudziŵa choipa chimene chidzaoneke pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gawira asanu ndi awiri ngakhale asanu ndi atatu; pakuti sudziwa choipa chanji chidzaoneka pansi pano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndalama zako uzisungitse kwa anthu asanu ndi awiri, inde kwa anthu asanu ndi atatu, pakuti sudziwa ndi tsoka lanji limene likubwera pa dziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gawira asanu ndi awiri ngakhale asanu ndi atatu; pakuti sudziwa coipa canji cidzaoneka pansi pano.