Ecclesiastes 11:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitambo ikadzaza ndi madzi, kumagwa mvula. Mtengo ukagwera chakumwera kapena chakumpoto, kumene wagwerako kogonera nkomweko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mitambo ikadzala mvula, itsanulira pansi; mtengo ukagwa kumwera pena kumpoto, pomwe unagwa mtengowo udzakhala pomwepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mitambo yadzaza ndi madzi, imagwetsa mvula pa dziko lapansi. Mtengo ukagwera cha kummwera kapena cha kumpoto, ndiye kuti udzagonera kumene wagwerako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mitambo ikadzala mvula, itsanulira pansi; mtengo ukagwa kumwela pena kumpoto, pomwe unagwa mtengowo udzakhala pomwepo.