Ecclesiastes 12:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi ya ukalamba wako, dzuŵa, kuŵala, mwezi, nyenyezi, zonse zidzakudera, ndipo mitambo idzabweranso mvula itagwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngakhale lisanade dzuwa, ndi kuunika, ndi mwezi, ndi nyenyezi, mitambo ndi kubweranso italeka mvula;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthawi ya ukalamba wako, dzuwa ndi kuwala, mwezi ndi nyenyezi zidzada. Mitambo idzabweranso mvula itagwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngakhale lisanade dzuwa, ndi kuunika, ndi mwezi, ndi nyenyezi, mitambo ndi kubweranso italeka mvula;