Ecclesiastes 12:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Makutu ako adzatsekeka ndipo sudzamva phokoso lakunja. Sudzamvanso kusinja kwapamtondo kapena kulira kwa mbalame m'mamaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pa khomo lakunja padzatsekeka; potsika mau akupera, wina nanyamuka polira mbalame, ndipo akazi onse akuimba sadzamveka bwino;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Makutu ako adzatsekeka, ndipo sudzamva phokoso lakunja; sudzamvanso kusinja kwa pa mtondo kapena kulira kwa mbalame mmawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pa khomo lakunja padzatsekeka; potsika mau akupera, wina nanyamuka polira mbalame, ndipo akazi onse akuyimba sadzamveka bwino;