Ecclesiastes 2:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidayamba kutaya mtima chifukwa cha ntchito zonse zimene ndidazigwira movutikira pansi pano.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinatembenuka ndi kukhululuka za ntchito zanga zonse ndasauka nazo kunja kuno.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Motero ndinayamba kutaya mtima chifukwa cha ntchito zonse zimene ndinazivutikira pansi pano.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinatembenuka ndi kukhululuka za nchito zanga zonse ndasauka nazo kunja kuno.