Ecclesiastes 2:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaachita ntchito zazikulu. Ndidaamanga nyumba zambiri, ndi kudziwokera mipesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinadzipangira zazikulu; ndinadzimangira nyumba; ndi kuoka mipesa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinagwira ntchito zikuluzikulu: Ndinadzimangira nyumba ndi kuwoka mipesa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinadzipangira zazikuru; ndinadzimangira nyumba; ndi kunka mipesa;