Ecclesiastes 5:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Masiku ake onse moyo wake unali wodzaza ndi mdima ndi chisoni, unali moyo wa mavuto, matenda ndi nkhaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde masiku ake onse amadya mumdima, nizimchulukira chisoni ndi nthenda ndi mkwiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masiku ake onse ndi odzaza ndi mdima, kukhumudwa kwakukulu, masautso ndi nkhawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde masiku ace onse amadya mumdima, nizimcurukira cisoni ndi nthenda ndi mkwiyo.