Ecclesiastes 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Alimi onse amatengako dzinthu dzam'minda, koma ndi mfumu yokha imene imaona phindu lake la mindayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phindutu la dziko lipindulira onse; ngakhale mfumu munda umthandiza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse amatengako zokolola za mʼminda: koma ndi mfumu yokha imene imapeza phindu la mindayi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phindutu la dziko lipindulira onse; ngakhale mfumu munda umthandiza.