Ecclesiastes 7:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkwabwino kuti utsate njira imodzi, komanso osataya njira inayo. Munthu woopa Mulungu adzapeza phindu ndi ziŵiri zonsezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuli kwabwino kugwira ichi; indetu, usachotsepo dzanja lako pakuti yemwe aopa Mulungu adzatuluka monsemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼkwabwino kuti utsate njira imodzi, ndipo usataye njira inayo. Munthu amene amaopa Mulungu adzapewa zinthu ziwiri zonsezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuli kwabwino kugwira ici; indetu, usacotsepo dzanja lako pakuti yemwe aopa Mulungu adzaturuka monsemo.