Ecclesiastes 7:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, pa dziko lapansi palibe munthu amene amachita zabwino zokhazokha osachimwa konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti kulibe wolungama pansi pano amene achita zabwino osachimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Palibe munthu wolungama pa dziko lapansi amene amachita zabwino zokhazokha ndipo sachimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti kulibe wolungama pansi pano amene acita zabwino osacimwa.