Ecclesiastes 7:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumtima mwako ukudziŵa kuti iweyonso udatukwanapo anthu ena.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti kawirikawiritu mtima wako udziwa kuti nawenso unatemberera ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti iwe ukudziwa mu mtima mwako kuti nthawi zambiri iwenso unatukwanapo ena.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti kawiri kawiritu mtima wako udziwa kuti nawenso unatemberera ena.