Ecclesiastes 7:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zonsezi ndidaziyesa ndi nzeru zanga. Ndinkati, “Ndidzakhala wanzeru.” Koma nzeruzo zinali nane kutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndayesa zonsezi ndi nzeru; ndinati, Ndidzakhala wanzeru; koma inanditalikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zonsezi ndinaziyesa ndi nzeru zanga ndipo ndinati, “Ine ndatsimikiza mu mtima mwanga kuti ndikhale wanzeru,” koma nzeruyo inanditalikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndayesa zonsezi ndi nzeru; ndinati, Ndidzakhala wanzeru, koma inanditarikira.