Ecclesiastes 7:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezitu nzimene ndidazipeza pakusonkhanitsa izi ndi izi, kuti ndidziŵe m'mene zinthu zimakhalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ichi ndachipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza chinthu china ndi chinzake, ndikazindikire malongosoledwe ao;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mlaliki akunena kuti, “Taonani, chimene ndinachipeza ndi ichi: “Kuwonjezera chinthu china pa china kuti ndidziwe mmene zinthu zimachitikira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ici ndacipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza cinthu cina ndi cinzace, ndikazindikire malongosoledwe ao;