Ecclesiastes 7:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndizo zimene mtima wanga unkazifunafuna kaŵirikaŵiri, koma osazipeza. Ndidapeza mwamuna mmodzi yekha wolungama pakati pa anthu 1,000, koma mkazi wolungama sindidampezepo ndi mmodzi yemwe pakati pa anthu onsewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chomwe moyo wanga uchifuna chifunire, koma osachipezai ndi ichi, mwamuna mmodzi mwa chikwi ndinampezadi, koma mkazitu mwa onsewo sindinampeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamene ine ndinali kufufuzabe koma osapeza kanthu, ndinapeza munthu mmodzi wolungama pakati pa anthu 1,000, koma pakati pawo panalibepo mkazi mmodzi wolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
comwe moyo wanga ucifuna cifunire, koma osacipezai ndi ici, mwamuna mmodzi mwa cikwi ndinampezadi, koma mkazitu mwa onsewo sindinampeza.