Ecclesiastes 7:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chisoni nchabwino kupambana chimwemwe, chifukwa ngakhale nkhope ikhale yakugwa, mtima umathabe kutolapo nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chisoni chiposa kuseka; pakuti nkhope yakugwa ikonza mtima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chisoni nʼchabwino kusiyana ndi kuseka, pakuti nkhope yakugwa ndi yabwino chifukwa imakonza mtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cisoni ciposa kuseka; pakuti nkhope yakugwa ikonza mtima.