Ecclesiastes 7:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuli bwino kuti munthu azimva kudzudzula kwa anthu anzeru, kupambana kumvera nyimbo zotamanda za zitsiru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumva chidzudzulo cha anzeru kupambana kumva nyimbo ya zitsiru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuli bwino kumva kudzudzula kwa munthu wanzeru kusiyana ndi kumvera mayamiko a zitsiru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumva cidzudzulo ca anzeru kupambana kumva nyimbo ya zitsiru.