Ecclesiastes 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma oipawo zinthu sizidzaŵayendera bwino, ndipo moyo wao udzakhala wosakhalitsa ngati mthunzi, poti samvera Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma woipa sadzapeza bwino ngakhale kutanimphitsa masiku ake ngati mthunzi; chifukwa saopa pamaso pa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma popeza oyipa saopa Mulungu zinthu sizidzawayendera bwino, ndipo moyo wawo sudzakhalitsa monga mthunzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma woipa sadzapeza bwino ngakhale kutanimphitsa masiku ace ngati mthunzi; cifukwa saopa pamaso pa Mulungu.