Ecclesiastes 8:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkaikapo mtima kuti ndidziŵe nzeru ndi kumvetsa ntchito zimene zikuchitika pansi pano, osapeza tulo usana ndi usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pompo ndinapereka mtima wanga kudziwa nzeru, ndi kupenya ntchito zichitidwa pansi pano; kuti anthu saona tulo konse ndi maso ao ngakhale usana ngakhale usiku;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndinayikapo mtima wanga kuti ndidziwe nzeru ndi kuonetsetsa ntchito za munthu pa dziko lapansi, osapeza tulo usana ndi usiku,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pompo ndinapereka mtima wanga kudziwa nzeru, ndi kupenya nchito zicitidwa pansi pano; kuti anthu saona tulo konse ndi maso ao ngakhale usana ngakhale usiku;