Ecclesiastes 9:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau a munthu wanzeru, olankhula mofatsa, ndi abwino kupambana kufuula kwa mfumu pa gulu la zitsiru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a anzeru achete amveka koposa kufuula kwa wolamulira mwa zitsiru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu oyankhula mofatsa a munthu wanzeru, anthu amawasamalira kwambiri kupambana kufuwula kwa mfumu ya zitsiru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a anzeru acete amveka koposa kupfuula kwa wolamulira mwa zitsiru.