Ecclesiastes 9:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nzeru nzabwino kupambana zida zankhondo, koma wochimwa mmodzi amatha kuwononga zabwino zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nzeru ipambana zida za nkhondo; koma wochimwa mmodzi aononga zabwino zambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nzeru ndi yabwino kupambana zida zankhondo, koma wochimwa mmodzi amawononga zinthu zambiri zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nzeru ipambana zida za nkhondo; koma wocimwa mmodzi aononga zabwino zambiri.