Ephesians 2:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu sapulumuka chifukwa cha ntchito zake, kuwopa kuti angamanyade.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chosachokera kuntchito, kuti asadzitamandire munthu aliyense.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
osati ndi ntchito, kuti wina aliyense asadzitamandire.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cosacokera kunchito, kuti asadzitamandire munthu ali yense.