Ephesians 3:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake tsono ndikugwadira Atate,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha ichi ndipinda maondo anga kwa Atate,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake ine ndikugwada pamaso pa Atate,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca ici ndipinda maondo anga kwa Atate,