Ephesians 3:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
amene banja lililonse Kumwamba ndi pansi pano limatchulidwa ndi dzina lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amene kuchokera kwa Iye fuko lonse la m'mwamba ndi la padziko alitcha dzina,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene banja lililonse kumwamba ndi pa dziko lapansi limatchulidwa ndi dzina lawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amene kucokera kwa iye pfuko lonse la m'mwamba ndi la padziko alicha dzina,