Ephesians 3:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumva mudamva za ntchito imene mwa ufulu wake Mulungu adandipatsa, yolalika pakati panu za kukoma mtima kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngatitu munamva za udindo wa chisomo cha Mulungu chimene anandipatsa ine cha kwa inu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithudi, inu munamva za ntchito yachisomo cha Mulungu imene anandipatsa chifukwa cha inu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ngatitu munamva za udindo wa cisomo ca Mulungucimene anandipatsa ine ca kwa inu;